Danieli 9:1 - Buku Lopatulika1 Chaka choyamba cha Dariusi mwana wa Ahasuwero, wa mbeu ya Amedi, amene anamlonga mfumu ya Ababiloni; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Chaka choyamba cha Dariusi mwana wa Ahasuwero, wa mbeu ya Amedi, amene anamlonga mfumu ya Ababiloni; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mʼchaka choyamba cha Dariyo mwana wa Ahasiwero (wochokera kwa Amedi), amene anakhala mfumu ya ku Babuloni, Onani mutuwo |