Danieli 6:28 - Buku Lopatulika28 Momwemo Daniele amene anakuzikabe pokhala Dariusi mfumu, ndi pokhala mfumu Kirusi wa ku Persiya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Momwemo Daniele amene anakuzikabe pokhala Dariusi mfumu, ndi pokhala mfumu Kirusi wa ku Persiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Choncho Danieli anapeza ufulu pa nthawi ya ulamuliro wa Dariyo ndi ulamuliro wa Koresi wa ku Perisiya. Onani mutuwo |