Danieli 6:27 - Buku Lopatulika27 Iye apulumutsa, nalanditsa, nachita zizindikiro ndi zozizwa m'mwamba ndi padziko lapansi, ndiye amene anapulumutsa Daniele kumphamvu ya mikango. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Iye apulumutsa, nalanditsa, nachita zizindikiro ndi zozizwa m'mwamba ndi pa dziko lapansi, ndiye amene anapulumutsa Daniele kumphamvu ya mikango. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Iye amalanditsa ndipo amapulumutsa, amachita zizindikiro ndi zozizwitsa kumwamba ndi pa dziko lapansi. Iye walanditsa Danieli ku mphamvu ya mikango.” Onani mutuwo |