Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Danieli 5:26 - Buku Lopatulika

26 Kumasulira kwake kwa mau awa ndi uku: MENE, Mulungu anawerenga ufumu wanu, nautha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Kumasulira kwake kwa mau awa ndi uku: MENE, Mulungu anawerenga ufumu wanu, nautha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 “Zimene mawuwa akutanthauza ndi izi: Mene: Mulungu wawerenga masiku a ufumu wanu ndipo wauthetsa.

Onani mutuwo Koperani




Danieli 5:26
11 Mawu Ofanana  

Atafa munthu, adzakhalanso ndi moyo kodi? Ndikadayembekeza masiku onse a nkhondo yanga, mpaka kwafika kusandulika kwanga.


Taonani, ndidzawautsira Amedi, amene sadzasamalira siliva, ngakhale golide sadzakondwera naye.


Ndipo amitundu onse adzamtumikira iye, ndi mwana wake, ndi mdzukulu wake, mpaka yafika nthawi ya dziko lake; ndipo amitundu ambiri ndi mafumu aakulu adzamuyesa iye mtumiki wao.


Ndipo lemba lolembedwa ndi ili: MENE MENE TEKEL ndi PARSIN.


chaka choyamba cha ufumu wake, ine Daniele ndinazindikira mwa mabuku kuti chiwerengo chake cha zaka, chimene mau a Yehova anadzera nacho kwa Yeremiya mneneri, kunena za makwaniridwe a mapasuko a Yerusalemu, ndizo zaka makumi asanu ndi awiri.


ati Ambuye, amene azidziwitsa zinthu zonsezo chiyambire dziko lapansi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa