Danieli 2:43 - Buku Lopatulika43 Ndi umo mudaonera chitsulo chosakanizika ndi dongo, iwo adzadzisokoneza ndi ana a anthu wamba; koma sadzaphatikizana, monga umo chitsulo sichimasakanizikana ndi dongo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Ndi umo mudaonera chitsulo chosanganizika ndi dongo, iwo adzadzisokoneza ndi ana a anthu wamba; koma sadzaphatikizana, monga umo chitsulo sichimasanganizikana ndi dongo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Ndipo monga munaona chitsulo chosakanizidwa ndi dongo, choncho anthu adzakhala wosakanizana ndipo sadzagwirizana, monga muja chitsulo sichingasakanizike ndi dongo. Onani mutuwo |