Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Danieli 2:43 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

43 Ndipo monga munaona chitsulo chosakanizidwa ndi dongo, choncho anthu adzakhala wosakanizana ndipo sadzagwirizana, monga muja chitsulo sichingasakanizike ndi dongo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

43 Ndi umo mudaonera chitsulo chosakanizika ndi dongo, iwo adzadzisokoneza ndi ana a anthu wamba; koma sadzaphatikizana, monga umo chitsulo sichimasakanizikana ndi dongo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

43 Ndi umo mudaonera chitsulo chosanganizika ndi dongo, iwo adzadzisokoneza ndi ana a anthu wamba; koma sadzaphatikizana, monga umo chitsulo sichimasanganizikana ndi dongo.

Onani mutuwo Koperani




Danieli 2:43
2 Mawu Ofanana  

Monga zala zinali za chitsulo chosakaniza ndi dongo, choncho ufumu uwu udzakhala pangʼono wolimba ndi pangʼono wofowoka.


“Pa nthawi ya mafumu amenewo, Mulungu wakumwamba adzakhazikitsa ufumu umene sudzawonongedwa, kapenanso kuperekedwa kwa anthu ena. Udzawononga maufumu onse aja ndi kuwatheratu, koma iwo wokha udzakhalapobe mpaka muyaya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa