Danieli 2:16 - Buku Lopatulika16 Nalowa Daniele, nafunsa mfumu amuikire nthawi, kuti aululire mfumu kumasulira kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Nalowa Daniele, nafunsa mfumu amuikire nthawi, kuti aululire mfumu kumasulira kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Danieli anapita mofulumira kwa mfumu ndipo anamupempha kuti amupatse nthawi kuti amuwuze zimene walota ndi tanthauzo lake. Onani mutuwo |