Danieli 2:17 - Buku Lopatulika17 Pamenepo Daniele anapita kunyumba kwake, nadziwitsa anzake Hananiya, Misaele, ndi Azariya, chinthuchi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pamenepo Daniele anapita kunyumba kwake, nadziwitsa anzake Hananiya, Misaele, ndi Azariya, chinthuchi; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Kenaka Danieli anabwerera ku nyumba kwake ndi kukafotokozera anzake aja zimenezi: Hananiya, Misaeli ndi Azariya. Onani mutuwo |