Danieli 11:44 - Buku Lopatulika44 Koma mbiri yochokera kum'mawa ndi kumpoto idzamvuta; nadzatuluka iye ndi ukali waukulu kupha ndi kuononga konse ambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Koma mbiri yochokera kum'mawa ndi kumpoto idzamvuta; nadzatuluka iye ndi ukali waukulu kupha ndi kuononga konse ambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Koma uthenga wochokera kummawa ndi kumpoto udzayiopsa, ndipo idzapita ndi ukali kukawononga ndi kutheratu anthu ambiri. Onani mutuwo |