Danieli 10:5 - Buku Lopatulika5 ndinakweza maso anga, ndinapenya ndi kuona munthu wovala bafuta, womanga m'chuuno ndi golide woona wa ku Ufazi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndinakweza maso anga, ndinapenya ndi kuona munthu wovala bafuta, womanga m'chuuno ndi golide woona wa ku Ufazi; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 ndinakweza maso ndipo ndinaona kuti pafupi ndi ine panali munthu wochokera ku Ufazi atavala zovala zosalala ndi lamba wa golide woyengeka bwino mʼchiwuno mwake. Onani mutuwo |