Danieli 10:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 ndinakweza maso ndipo ndinaona kuti pafupi ndi ine panali munthu wochokera ku Ufazi atavala zovala zosalala ndi lamba wa golide woyengeka bwino mʼchiwuno mwake. Onani mutuwoBuku Lopatulika5 ndinakweza maso anga, ndinapenya ndi kuona munthu wovala bafuta, womanga m'chuuno ndi golide woona wa ku Ufazi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndinakweza maso anga, ndinapenya ndi kuona munthu wovala bafuta, womanga m'chuuno ndi golide woona wa ku Ufazi; Onani mutuwo |