Danieli 1:12 - Buku Lopatulika12 Muyesetu anyamata anu masiku khumi; atipatse zomera m'nthaka tidye, ndi madzi timwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Muyesetu anyamata anu masiku khumi; atipatse zomera m'nthaka tidye, ndi madzi timwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 “Chonde mutiyese ife akapolo anu pa masiku khumi: mutipatse masamba okha kuti tidye ndi madzi akumwa. Onani mutuwo |