Amosi 8:7 - Buku Lopatulika7 Yehova walumbira pali kudzikuza kwa Yakobo, Ngati ndidzaiwala konse ntchito zao zilizonse? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Yehova walumbira pali kudzikuza kwa Yakobo, Ngati ndidzaiwala konse ntchito zao zilizonse? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Chauta, Mulungu amene ana a Yakobe amamnyadira walumbira kuti, “Ndithudi, sindidzaiŵala zochita zao zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Yehova amene Yakobo amamunyadira, walumbira kuti: Ine sindidzayiwala chilichonse chimene anachita. Onani mutuwo |