Amosi 7:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Yehova anachileka. Ichi chomwe sichidzachitika, ati Ambuye Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Yehova anachileka. Ichi chomwe sichidzachitika, ati Ambuye Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Apo Chauta adakhululuka, ndipo adati, “Zimenezinso sizidzachitika konse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kotero Yehova anakhululuka. Ambuye Yehova anati, “Izinso sizidzachitika.” Onani mutuwo |