Amosi 7:5 - Buku Lopatulika5 Pamenepo ndinati, Ambuye Yehova, lekanitu; Yakobo adzakhala chilili bwanji? Pakuti ali wamng'ono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pamenepo ndinati, Ambuye Yehova, lekanitu; Yakobo adzakhala chilili bwanji? Pakuti ali wamng'ono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsono ine ndidati, “Inu Ambuye Chauta, ndapota nanu, basi lekani. Kodi anthu a Yakobeŵa angalimbike bwanji? Iwoŵa ndi ofooka kwambiri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Tsono ine ndinafuwula kuti, “Ambuye Yehova, chonde ndikukupemphani, lekani! Kodi Yakobo adzapulumuka bwanji? Iye ndi wofowoka kwambiri!” Onani mutuwo |