Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Amosi 6:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo kudzachitika, mukatsala amuna khumi m'nyumba imodzi, adzafa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo kudzachitika, mukatsala amuna khumi m'nyumba imodzi, adzafa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Anthu khumi akadzakhala akubisala m'nyumba imodzi, nawonso adzafabe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ngati anthu khumi otsala adzabisala mʼnyumba imodzi, nawonso adzafa ndithu.

Onani mutuwo Koperani




Amosi 6:9
10 Mawu Ofanana  

Nawawerengera Hamani kulemera kwake kwakukulu, ndi ana ake ochuluka, ndi zonse mfumu idamkuza nazo, ndi umo adamkweza koposa akalonga ndi anyamata a mfumu.


ana aamuna khumi a Hamani mwana wa Hamedata, mdani wa Ayuda. Koma sanalande zofunkha.


ndipo taonani, inadza mphepo yaikulu yochokera kuchipululu, niomba pangodya zonse zinai za nyumbayo, nigwa pa anyamatawo, nafa; ndipo ndapulumuka ine ndekha kudzakuuzani.


Ndipo anabala ana aamuna asanu ndi awiri, ndi ana aakazi atatu.


Phindu la m'nyumba mwake lidzachoka, akatundu ake adzamthawa tsiku la mkwiyo wake.


Zidzukulu zake zidulidwe; dzina lao lifafanizidwe mu mbadwo ukudza.


Konzani inu popherapo ana ake, chifukwa cha kuipa kwa atate ao; kuti iwo asadzuka ndi kukhala nalo dziko, ndi kudzaza dziko lapansi ndi mizinda.


Pakuti imfa yakwera m'mazenera athu, yalowa m'nyumba mwathu; kuchotsa ana kubwalo, ndi anyamata kumiseu.


Pakuti atero Ambuye Yehova, M'nyumba ya Israele, mzinda wotulukamo chikwi chimodzi adzautsalira zana limodzi, ndi uwu wotulukamo zana limodzi adzautsalira khumi.


Ndipo munthu wako, amene ndidzamleka osamlikha paguwa langa la nsembe, adzatha maso ako, ndi kumvetsa mtima wako chisoni; ndipo obadwa onse a m'banja lako adzamwalira akali biriwiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa