Amosi 3:7 - Buku Lopatulika7 Pakuti Ambuye Yehova sadzachita kanthu osawulula chinsinsi chake kwa atumiki ake aneneri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pakuti Ambuye Yehova sadzachita kanthu osawulula chinsinsi chake kwa atumiki ake aneneri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Zoonadi, Ambuye Chauta sachita kanthu osadziŵitsa atumiki ao, aneneri, zimene akonzekera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Zoonadi Ambuye Yehova sachita kanthu asanawulule zimene akufuna kuchita kwa atumiki ake, aneneri. Onani mutuwo |