Amosi 3:5 - Buku Lopatulika5 Kodi mbalame idzakodwa mumsampha pansi popanda msampha woitchera? Kodi msampha ufwamphuka pansi wosakola kanthu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Kodi mbalame idzakodwa mumsampha pansi popanda msampha woitchera? Kodi msampha ufwamphuka pansi wosakola kanthu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Kodi mbalame nkukatera pa msampha pansi, popanda nyambo yake? Nanga msamphawo kodi nkufwamphuka pansipo, usanakole kanthu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Kodi mbalame nʼkutera pa msampha pamene palibe nyambo yake? Kodi msampha umafwamphuka usanakole kanthu? Onani mutuwo |