Amosi 3:4 - Buku Lopatulika4 Kodi mkango udzabangula m'nkhalango wosakhala nayo nyama? Kodi msona wa mkango udzalira m'ngaka mwake usanagwire kanthu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Kodi mkango udzabangula m'nkhalango wosakhala nayo nyama? Kodi msona wa mkango udzalira m'ngaka mwake usanagwire kanthu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Kodi mkango umabangula m'nkhalango, usanagwire nyama? Kodi msona wa mkango umakhuluma m'phanga mwake, usanagwire kanthu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kodi mkango umabangula mʼnkhalango usanagwire nyama? Kodi msona wamkango umalira mʼphanga mwake pamene sunagwire kanthu? Onani mutuwo |