Amosi 3:3 - Buku Lopatulika3 Kodi awiri adzayenda pamodzi asanapanganiranetu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Kodi awiri adzayenda pamodzi asanapanganiranetu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 “Kodi anthu aŵiri nkuyendera pamodzi, osapangana? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kodi anthu awiri nʼkuyendera limodzi asanapangane? Onani mutuwo |