Amosi 1:3 - Buku Lopatulika3 Atero Yehova, Chifukwa cha zolakwa zitatu za Damasiko, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwake; popeza anapuntha Giliyadi ndi zopunthira zachitsulo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Atero Yehova, Chifukwa cha zolakwa zitatu za Damasiko, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwake; popeza anapuntha Giliyadi ndi zopunthira zachitsulo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Zimene akunena Chauta ndi izi: “Chifukwa anthu a ku Damasiko akunka nachimwirachimwira, sindileka kuŵalanga. Iwo ankazunza anthu a ku Giliyadi mwankhanza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Yehova akuti, “Chifukwa anthu a ku Damasiko akunka nachimwirachimwira, Ine sindileka kuwalanga. Popeza anapuntha Giliyadi ndi zopunthira za mano achitsulo, Onani mutuwo |