Akolose 4:15 - Buku Lopatulika15 Perekani moni kwa abalewo a mu Laodikea, ndi Nimfa, ndi Mpingowo wa m'nyumba yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Akupatsani moni abalewo a m'Laodikea, ndi Nimfa, ndi Mpingowo wa m'nyumba yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mutiperekereko moni kwa abale athu okhala ku Laodikea, ndiponso kwa Nimfa ndi kwa ampingo amene amasonkhana kunyumba kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Perekani moni kwa abale a ku Laodikaya, ndiponso kwa Numfa ndi mpingo wa mʼnyumba mwake. Onani mutuwo |