Akolose 4:14 - Buku Lopatulika14 Akupatsani moni Luka sing'anga wokondedwa, ndi Dema. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Akupatsani moni Luka sing'anga wokondedwa, ndi Dema. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Luka, sing'anga wathu wokondedwa, ndiponso Dema, onsewo akuti moni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Luka, dotolo wathu wokondedwa ndi Dema, akupereka moni. Onani mutuwo |