Akolose 4:13 - Buku Lopatulika13 Pakuti ndimchitira iye umboni kuti adziwawitsa nayo ntchito chifukwa cha inu, ndi iwo a mu Laodikea, ndi iwo a mu Hierapoli. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pakuti ndimchitira iye umboni kuti adziwawitsa nayo ntchito chifukwa cha inu, ndi iwo a m'Laodikea, ndi iwo a m'Hierapoli. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ndingathe kumchitira umboni kuti amagwira ntchito kwambiri chifukwa cha inu, ndiponso chifukwa cha anthu okhala ku Laodikea ndi ku Hierapoli. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ine ndikumuchitira umboni kuti amagwira ntchito mwamphamvu chifukwa cha inu ndiponso kwa amene ali ku Laodikaya ndi Herapoli. Onani mutuwo |