Akolose 3:25 - Buku Lopatulika25 Pakuti iye wakuchita chosalungama adzalandiranso chosalungama anachitacho; ndipo palibe tsankho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pakuti iye wakuchita chosalungama adzalandiranso chosalungama anachitacho; ndipo palibe tsankho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Koma munthu amene amachita zosalungama, zidzamubwerera, chifukwa Mulungu amaweruza mosakondera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Aliyense amene amachita zolakwa adzalandira malipiro molingana ndi kulakwa kwake, ndipo palibe tsankho. Onani mutuwo |