Akolose 3:19 - Buku Lopatulika19 Amuna inu, kondani akazi anu, ndipo musawawire mtima iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Amuna inu, kondani akazi anu, ndipo musawawire mtima iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Inu amuna, muzikonda akazi anu, musamaŵavutitse ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Inu amuna, kondani akazi anu ndipo musawapsere mtima. Onani mutuwo |