Akolose 1:4 - Buku Lopatulika4 popeza tidamva za chikhulupiriro chanu cha mwa Khristu Yesu, ndi chikondi muli nacho kwa oyera mtima onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 popeza tidamva za chikhulupiriro chanu cha mwa Khristu Yesu, ndi chikondi muli nacho kwa oyera mtima onse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Timathokoza chifukwa tamva kuti mumakhulupirira Khristu Yesu, ndiponso kuti mumakonda anthu onse a Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Timayamika chifukwa tinamva za chikhulupiriro chanu mwa Khristu Yesu ndi za chikondi chanu pa oyera mtima onse. Onani mutuwo |