Akolose 1:3 - Buku Lopatulika3 Tiyamika Mulungu Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu ndi kupempherera inu nthawi zonse, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Tiyamika Mulungu Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu ndi kupempherera inu nthawi zonse, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tikamakupemphererani, nthaŵi zonse timathokoza Mulungu, Atate a Ambuye athu Yesu Khristu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Timayamika Mulungu Atate wa Ambuye athu Yesu Khristu, nthawi zonse pamene tikukupemphererani. Onani mutuwo |