Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 9:18 - Buku Lopatulika

18 momwemo choyambachonso sichinakonzeke chopanda mwazi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 momwemo choyambachonso sichinakonzeka chopanda mwazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Nchifukwa chake ngakhale Chipangano choyamba chija sichidachitike popanda kukhetsa magazi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Nʼchifukwa chake pangano loyamba lija silinachitike popanda kukhetsa magazi.

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 9:18
8 Mawu Ofanana  

Ndipo muzitenga mpukutu wa hisope, ndi kuuviika m'mwazi uli m'mbale, ndi kupaka mwazi uli m'mbalemo pa mphuthu ya pamwamba ndi pambali; koma inu, asatuluke munthu pakhomo pa nyumba yake kufikira m'mawa.


Pamenepo anabwera nao ana aamuna a Aroni, ndi Mose anatengako mwazi, naupaka pa ndewerere ya khutu lao la ku dzanja lamanja, ndi pa chala chachikulu cha ku dzanja lamanja lao, ndi pa chala chachikulu cha phazi lao la ku dzanja lamanja; ndipo Mose anawaza mwaziwo paguwa la nsembe pozungulira.


koposa kotani nanga mwazi wa Khristu amene anadzipereka yekha wopanda chilema kwa Mulungu mwa Mzimu wosatha, udzayeretsa chikumbumtima chanu kuchisiyanitsa ndi ntchito zakufa, kukatumikira Mulungu wamoyo?


Pakuti chopangiratu chiona mphamvu atafa mwini wake; popeza chilibe mphamvu konse pokhala wolemberayo ali ndi moyo;


Pakuti pamene Mose adalankhulira anthu onse lamulo lililonse monga mwa chilamulo, anatenga mwazi wa anaang'ombe ndi mbuzi, pamodzi ndi madzi ndi ubweya wofiira ndi hisope, nawaza buku lomwe, ndi anthu onse,


Ndipo monga mwa chilamulo zitsala zinthu pang'ono zosayeretsedwa ndi mwazi, ndipo wopanda kukhetsa mwazi palibe kukhululukidwa kwa machimo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa