Ahebri 9:17 - Buku Lopatulika17 Pakuti chopangiratu chiona mphamvu atafa mwini wake; popeza chilibe mphamvu konse pokhala wolemberayo ali ndi moyo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pakuti chopangiratu chiona mphamvu atafa mwini wake; popeza chilibe mphamvu konse pokhala wolemberayo ali ndi moyo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Paja chipangano chotere chilibe mphamvu, asanamwalire wochilemba. Chimakhala ndi mphamvu pokhapokha wochilembayo atamwalira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 chifukwa pangano lotere limakhala ndi mphamvu ngati wolembayo wamwalira. Siligwira ntchito pamene wolembayo ali ndi moyo. Onani mutuwo |