Ahebri 9:16 - Buku Lopatulika16 Pakuti pamene pali chopangiratu pafunika pafike imfa ya wolemberayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pakuti pamene pali chopangiratu pafunika pafike imfa ya wolemberayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ngati munthu alemba Chipangano chosiyira ena chuma, pafunika kutsimikiza kuti wolemba chipanganocho wamwaliradi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ngati munthu alemba pangano losiyira ena chuma, pafunika kutsimikiza kuti wolemba panganolo wamwaliradi, Onani mutuwo |