Ahebri 8:2 - Buku Lopatulika2 Mtumiki wa malo opatulika, ndi wa chihema choona, chimene Ambuye anachimanga, si munthu ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mtumiki wa malo opatulika, ndi wa chihema choona, chimene Ambuye anachimanga, si munthu ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Iye akutumikira m'Malo Opatulika am'katikati, ndiye kuti m'chihema chenicheni chimene adachimanga ndi Ambuye osati munthu ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo akutumikira mʼmalo opatulika, mu Tenti yeniyeni yoyikidwa ndi Ambuye, osati ndi munthu. Onani mutuwo |