Ahebri 8:1 - Buku Lopatulika1 Koma mutu wa izi tanenazi ndi uwu: Tili naye Mkulu wa ansembe wotere, amene anakhala padzanja lamanja la mpando wachifumu wa Ukulu mu Kumwamba, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma mutu wa izi tanenazi ndi uwu: Tili naye Mkulu wa ansembe wotere, amene anakhala pa dzanja lamanja la mpando wachifumu wa Ukulu m'Kumwamba, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mfundo yeniyeni pa zimene tikunenazi ndi iyi: tili naye wotere Mkulu wa ansembe onse, amene akukhala ku dzanja lamanja la mpando wachifumu wa Mulungu Waulemerero Kumwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Fundo yayikulu pa zimene tikunenazi ndi iyi: Tili naye ife Mkulu wa ansembe, amene anakhala ku dzanja lamanja la mpando waufumu wa Mulungu Waulemerero kumwamba. Onani mutuwo |