Ahebri 8:12 - Buku Lopatulika12 Kuti ndidzachitira chifundo zosalungama zao, ndipo zoipa zao sindidzazikumbukanso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Kuti ndidzachitira chifundo zosalungama zao, ndipo zoipa zao sindidzazikumbukanso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Mwachifundo ndidzaŵakhululukira zochimwa zao, sindidzakumbukiranso machimo ao.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pakuti Ine ndidzawakhululukira zoyipa zawo, ndipo sindidzakumbukiranso machimo awo.” Onani mutuwo |