Ahebri 7:6 - Buku Lopatulika6 koma iye amene mawerengedwe a chibadwidwe chake sachokera mwa iwo, anatenga limodzi la magawo khumi kwa Abrahamu, namdalitsa iye amene ali nao malonjezano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 koma iye amene mawerengedwe a chibadwidwe chake sachokera mwa iwo, anatenga limodzi la magawo khumi kwa Abrahamu, namdalitsa iye amene ali nao malonjezano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Melkizedeki sanali m'gulu la zidzukulu za Levi, komabe adalandira chachikhumi kwa Abrahamu. Ndipo adadalitsa Abrahamu, munthu amene anali atalandira malonjezo a Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Melikizedeki sanali wochokera kwa Levi, komabe analandira chakhumi kuchokera kwa Abrahamu nadalitsa Abrahamuyo amene analandira malonjezo a Mulungu. Onani mutuwo |