Ahebri 7:4 - Buku Lopatulika4 Koma tapenyani ukulu wake wa iyeyu, amene Abrahamu, kholo lalikulu, anampatsa limodzi la magawo khumi la zosankhika za kunkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma tapenyani ukulu wake wa iyeyu, amene Abrahamu, kholo lalikulu, anampatsa limodzi la magawo khumi la zosankhika za kunkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mukuwonatu tsono kuti munthuyo anali wamkulu ndithu. Nanga Abrahamu, kholo lathu lija, kuchita kumpatsa chachikhumi cha zimene adaafunkha! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mukuona tsono kuti munthuyo anali wamkulu ndithu, pakuti Abrahamu kholo lathu anamupatsa chakhumi cha zimene anafunkha. Onani mutuwo |