Ahebri 7:18 - Buku Lopatulika18 Pakutitu kuli kutaya kwake kwa lamulo lidadza kalelo, chifukwa cha kufooka kwake, ndi kusapindulitsa kwake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pakutitu kuli kutaya kwake kwa lamulo lidadza kalelo, chifukwa cha kufooka kwake, ndi kusapindulitsa kwake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Motero lamulo lakale lalekeka chifukwa linali lopanda mphamvu, linali lopanda phindu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Choncho lamulo loyamba lachotsedwa chifukwa linali lofowoka ndi lopanda phindu. Onani mutuwo |