Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 7:17 - Buku Lopatulika

17 pakuti amchitira umboni, Iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha monga mwa dongosolo la Melkizedeki.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 pakuti amchitira umboni, Iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha monga mwa dongosolo la Melkizedeki.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Paja mau a Mulungu pomuchitira umboni akuti, “Ndiwe wansembe mpaka muyaya, unsembe wake wonga uja wa Melkizedeki.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Pakuti Mulungu anamuchitira umboni kuti, “Iwe ndi wansembe wamuyaya, monga mwa dongosolo la unsembe wa Melikizedeki.”

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 7:17
7 Mawu Ofanana  

Yehova walumbira, ndipo sadzasintha, Inu ndinu wansembe kosatha monga mwa chilongosoko cha Melkizedeki.


wotchedwa ndi Mulungu mkulu wa ansembe monga mwa dongosolo la Melkizedeki.


Monga anenanso mwina, Iwe ndiwe wansembe wa nthawi zonse monga mwa dongosolo la Melkizedeki.


m'mene Yesu mtsogoleri analowamo chifukwa cha ife, atakhala mkulu wa ansembe nthawi yosatha monga mwa dongosolo la Melkizedeki.


Ndipo pakadakhala ungwiro mwa unsembe wa Chilevi (pakuti momwemo anthu analandira chilamulo), pakadatsala kusowa kotani kuti auke wansembe wina monga mwa dongosolo la Melkizedeki, wosayesedwa monga mwa dongosolo la Aroni?


Ndipo kwadziwikatu koposa ndithu, ngati auka wansembe wina monga mwa mafanidwe a Melkizedeki,


koma Iye ndi lumbiro mwa Iye amene anenana kwa Iye, Walumbira Ambuye ndipo sadzalapa, iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha).


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa