Ahebri 7:12 - Buku Lopatulika12 Pakuti posandulika unsembe, kufunikanso kuti lamulo lisandulike. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pakuti posandulika unsembe, kufunikanso kuti lamulo lisandulike. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pakuti pakakhala kusintha pa unsembe, ndiye kuti pa Malamulonso sipangalephere kukhala kusintha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pakuti pamene unsembe usintha, malamulonso amayenera kusintha. Onani mutuwo |