Ahebri 7:10 - Buku Lopatulika10 pakuti pajapo anali m'chuuno cha atate wake, pamene Melkizedeki anakomana naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 pakuti pajapo anali m'chuuno cha atate wake, pamene Melkizedeki anakomana naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pakuti iye anali akadali m'thupi la kholo lake Abrahamu pamene Melkizedeki adadzamchingamira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 chifukwa pamene Melikizedeki anakumana ndi Abrahamu nʼkuti Levi ali mʼthupi la kholo lake. Onani mutuwo |