Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 7:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo kuli ngati kunena, mwa Abrahamu Levinso wakulandira limodzilimodzi la magawo khumi adapereka limodzi la magawo khumi;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo kuli ngati kunena, mwa Abrahamu Levinso wakulandira limodzilimodzi la magawo khumi adapereka limodzi la magawo khumi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Kwenikweni tingathe kunena kuti pamene Abrahamu ankapereka chachikhumi, Levi yemwe, amene amalandira chachikhumi, adaapereka nao chachikhumicho.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Wina angathe kunena kuti Levi, amene amalandira chakhumi, anapereka chakhumicho kudzera mwa Abrahamu,

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 7:9
7 Mawu Ofanana  

ayamikike Mulungu Wamkulukulu amene wapereka adani ako m'dzanja lako. Ndipo anampatsa iye limodzi la magawo khumi la zonse.


pakuti yense wakupempha alandira; ndi wakufunayo apeza; ndi kwa wogogodayo chitsegulidwa.


Chifukwa chake, monga uchimo unalowa m'dziko lapansi mwa munthu mmodzi, ndi imfa mwa uchimo; chotero imfa inafikira anthu onse, chifukwa kuti onse anachimwa.


Mutatha kugawa magawo khumi, zobala zanu zonse chaka chachitatu, ndicho chaka chogawa magawo khumi, muzizipereka kwa Mlevi, kwa mlendo, kwa mwana wamasiye, ndi kwa mkazi wamasiye, kuti adye m'midzi mwanu, ndi kukhuta.


pakuti pajapo anali m'chuuno cha atate wake, pamene Melkizedeki anakomana naye.


Koma tapenyani ukulu wake wa iyeyu, amene Abrahamu, kholo lalikulu, anampatsa limodzi la magawo khumi la zosankhika za kunkhondo.


Ndipo pano anthu ofeka alandira limodzi la magawo khumi; koma apo iye, woti adamchitira umboni kuti ali ndi moyo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa