Ahebri 5:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo palibe munthu adzitengera ulemuwo mwini wake, komatu iye amene aitanidwa ndi Mulungu, monga momwenso Aroni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo palibe munthu adzitengera ulemuwo mwini wake, komatu iye amene aitanidwa ndi Mulungu, monga momwenso Aroni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Palibe munthu amadzitengera yekha ulemu wokhala mkulu wa ansembe onse, koma amachita kuitanidwa ndi Mulungu, monga momwe adaaitanidwira Aroni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Palibe amene amadzipatsa yekha ulemu wotere, koma amachita kuyitanidwa ndi Mulungu monga momwe anayitanidwira Aaroni. Onani mutuwo |