Ahebri 5:11 - Buku Lopatulika11 Za iye tili nao mau ambiri kuwanena, ndi otivuta powatanthauzira, popeza mwagontha m'makutu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Za iye tili nao mau ambiri kuwanena, ndi otilaka powatanthauzira, popeza mwagontha m'makutu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tili ndi zambiri zoti nkunena pa zimenezi, koma nzovuta kufotokoza kwake, popeza kuti mwasanduka ouma mitu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tili ndi zambiri zoti tinganene pa zimenezi, koma ndi zovuta kukufotokozerani chifukwa ndinu ochedwa kuphunzira. Onani mutuwo |