Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 4:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo m'menemonso, Ngati adzalowa mpumulo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo m'menemonso, Ngati adzalowa mpumulo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Panonso akunena za zomwezo pamene akuti, “Sadzaloŵa konse mu mpumulo umene ndidaŵakonzera.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Pa ndime inonso akunena za zomwezo pamene akuti, “Iwo sadzalowa konse mu mpumulo wanga.”

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 4:5
3 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake ndinalumbira mu mkwiyo wanga, ngati adzalowa mpumulo wanga.


Monga ndinalumbira mu ukali wanga: Ngati adzalowa mpumulo wanga!


Popeza ife amene takhulupirira tilowa mpumulowo, monga momwe ananena, Monga ndalumbira mu mkwiyo wanga, ngati adzalowa mpumulo wanga. Zingakhale ntchitozo zidatsirizika kuyambira kuzika kwa dziko lapansi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa