Ahebri 4:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti wanena pena za tsiku lachisanu ndi chiwiri, natero, Ndipo Mulungu anapumula tsiku lachisanu ndi chiwiri, kuleka ntchito zake zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti wanena pena za tsiku lachisanu ndi chiwiri, natero, Ndipo Mulungu anapumula tsiku lachisanu ndi chiwiri, kuleka ntchito zake zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pena pake ponena za tsiku lachisanu ndi chiŵiri pali mau akuti, “Mulungu adapumula pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri, kuleka ntchito zake zonse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pena pake wayankhula za tsiku lachisanu ndi chiwiri mʼmawu awa: “Pa tsiku lachisanu ndi chiwiri, Mulungu anapumula ku ntchito zake zonse.” Onani mutuwo |
koma tsiku lachisanu ndi chiwiri ndilo Sabata la Yehova Mulungu wako; usamagwira ntchito iliyonse, iwe, kapena mwana wako wamwamuna, kapena mwana wako wamkazi, kapena wantchito wako wamwamuna, kapena wantchito wako wamkazi, kapena ng'ombe yako, kapena bulu wako, kapena zoweta zako zilizonse, kapena mlendo wokhala m'mudzi mwako; kuti wantchito wako wamwamuna ndi wantchito wako wamkazi apumule monga iwe mwini.