Ahebri 3:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti nyumba iliyonse ili naye wina woimanga; koma wozimanga zonse ndiye Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti nyumba iliyonse ili naye wina woimanga; koma wozimanga zonse ndiye Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Nyumba iliyonse imamangidwa ndi munthu wakutiwakuti, koma amene adapanga zonse, ndi Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pakuti nyumba iliyonse imamangidwa ndi munthu wina, koma amene anapanga zonse ndi Mulungu. Onani mutuwo |