Ahebri 3:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti ameneyo wayesedwa woyenera ulemerero woposa Mose, monga momwe iye amene anaimanga nyumba ali nao ulemerero woposa nyumbayi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti ameneyo wayesedwa woyenera ulemerero woposa Mose, monga momwe iye amene anaimanga nyumba ali nao ulemerero woposa nyumbayi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Munthu womanga nyumba amalandira ulemu woposa ulemerero wa nyumbayo. Momwemonso Yesu ngwoyenera kulandira ulemerero woposa ulemerero wa Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Yesu anapezeka woyenera kulandira ulemu waukulu kuposa Mose, monga momwemonso womanga nyumba amalandira ulemu waukulu kuposa nyumbayo. Onani mutuwo |