Ahebri 3:2 - Buku Lopatulika2 amene anakhala wokhulupirika kwa Iye adamuikayo, monganso Mose m'nyumba yake yonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 amene anakhala wokhulupirika kwa Iye adamuikayo, monganso Mose m'nyumba yake yonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Paja Iye anali wokhulupirika kwa Mulungu amene adampatsa udindowo, monga momwe Mosenso anali wokhulupirika m'nyumba yonse ya Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anali wokhulupirika kwa Mulungu amene anamupatsa udindowo, monga momwe Mose anali wokhulupirika mʼnyumba yonse ya Mulungu. Onani mutuwo |