Ahebri 3:10 - Buku Lopatulika10 Momwemo ndinakwiya nao mbadwo uwu, ndipo ndinati, Nthawi zonse amasochera mumtima; koma sanazindikire njira zanga iwowa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Momwemo ndinakwiya nao mbadwo uwu, ndipo ndinati, Nthawi zonse amasochera mumtima; koma sanazindikira njira zanga iwowa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono ndidaukwiyira mbadwowo, ndipo ndidati, ‘Nthaŵi zonse amasokera mumtima mwao, sanaphunzirebe njira zanga.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Nʼchifukwa chake ndinawukwiyira mʼbadowo, ndipo Ine ndinati, ‘Nthawi zonse mitima yawo imasochera, ndipo iwo sadziwa njira zanga.’ Onani mutuwo |