Ahebri 3:11 - Buku Lopatulika11 Monga ndinalumbira mu ukali wanga: Ngati adzalowa mpumulo wanga! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Monga ndinalumbira m'ukali wanga: Ngati adzalowa mpumulo wanga! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Motero ndili wokwiya ndidalumbira kuti, ‘Sadzaloŵa konse mu mpumulo umene ndidaŵakonzera.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kotero Ine ndinalumbira nditakwiya kuti, ‘Iwo sadzalowa mu mpumulo wanga.’ ” Onani mutuwo |